Genesis 37:32 - Buku Lopatulika32 natumiza malaya amwinjiro, nadza nao kwa atate ao: ndipo anati, Siwa tawatola; muzindikire tsono ngati ndi malaya a mwana wanu, kapena ndi ena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 natumiza malaya amwinjiro, nadza nao kwa atate ao: ndipo anati, Siwa tawatola; muzindikire tsono ngati ndi malaya a mwana wanu, kapena ndi ena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Adatenga mkanjowo napita nawo kwa bambo wao, nati, “Tayang'anani, kapena nkukhala mkanjo wa mwana wanu uja.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Iwo anatenga mkanjo uja nabwerera nawo kwa abambo awo nati, “Ife tapeza mkanjowu. Tawuyangʼanitsitsani muone ngati uli wa mwana wanu.” Onani mutuwo |