Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 37:31 - Buku Lopatulika

31 Ndipo anatenga malaya ake a Yosefe, napha tonde, naviika malaya m'mwazi wake:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Ndipo anatenga malaya ake a Yosefe, napha tonde, naviika malaya m'mwazi wake:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Pomwepo iwo adapha mbuzi, naviika mkanjo wa Yosefe uja m'magazi ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Tsono anapha kamwana ka mbuzi, natenga mkanjo wa Yosefe ndi kuwunyika mʼmagazi ake.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 37:31
6 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene Yosefe anafika kwa abale ake, anamvula Yosefe malaya ake, malaya amwinjiro amene anavala iye;


Koma Israele anamkonda Yosefe koposa ana ake onse, pakuti anali mwana wa ukalamba wake; ndipo anamsokera iye malaya amwinjiro.


natumiza malaya amwinjiro, nadza nao kwa atate ao: ndipo anati, Siwa tawatola; muzindikire tsono ngati ndi malaya a mwana wanu, kapena ndi ena.


wina anatuluka kwa ine ndipo ndinati, Zoonatu, wakadzulidwa; ndipo sindidzamuonanso iye;


Ndipo anamfotokozera iye kuti, Yosefe akali ndi moyo, ndipo alamulira m'dziko lonse la Ejipito. Pamenepo mtima wake unakomoka, pakuti sanawakhulupirire iwo.


Wobisa machimo ake sadzaona mwai; koma wakuwavomereza, nawasiya adzachitidwa chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa