Genesis 37:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo anazindikira nati, Ndiwo malaya a mwana wanga: wajiwa ndi chilombo: Yosefe wakadzulidwa ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo anazindikira nati, Ndiwo malaya a mwana wanga: wajiwa ndi chilombo: Yosefe wakadzulidwa ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Yakobe adauzindikira mkanjowo, nati, “Ha, ndi wakedi! Chilombo chamupha mwana wanga. Kalanga ine, Yosefe wakadzulidwa!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Iye anawuzindikira ndipo anati, “Ndi mkanjo wa mwana wanga umenewu! Nyama yakuthengo yolusa yamudya. Mosakayika, mwana wanga Yosefe wakhadzulidwa.” Onani mutuwo |