Genesis 37:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'chipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye m'manja mwao, ambwezenso kwa atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'chipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye m'manja mwao, ambwezenso kwa atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tingomuponya m'chitsime chopanda madzichi kuchipululu konkuno. Tisampweteke konse.” Ankanena zimenezi akuganiza zomupulumutsa m'manja mwao, kuti amtumize kwa bambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 tisakhetse magazi. Tiyeni timuponye mʼchitsime ku chipululu konkuno. Koma tisamuvulaze nʼkomwe. Rubeni ananena zonsezi kuti apulumutse Yosefe ndi kuti pambuyo pake akamupereke kwa abambo awo.” Onani mutuwo |