Genesis 37:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Rubeni anamva nampulumutsa iye m'manja mwao; nati, Tisamuphe iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Rubeni anamva nampulumutsa iye m'manja mwao; nati, Tisamuphe iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono Rubeni adamva zimene enawo ankanena, ndipo adayesetsa kumpulumutsa Yosefe. Adati, “Ai tisamuphe, tisakhetse magazi ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma Rubeni atamva izi, anapulumutsa Yosefe. Iye anati kwa abale ake, “Ayi, tisamuphe, Onani mutuwo |