Genesis 37:17 - Buku Lopatulika17 Munthuyo ndipo anati, Anachoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotani. Yosefe ndipo anatsata abale ake, nawapeza ali ku Dotani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Munthuyo ndipo anati, Anachoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotani. Yosefe ndipo anatsata abale ake, nawapeza ali ku Dotani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Munthuyo adati, “Adachoka kale kuno. Ndidaŵamva akunena kuti akupita ku Dotani.” Apo Yosefe adaŵalondola abale akewo, nakaŵapeza ku Dotani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Munthuyo anayankha nati, “Anasamukako kuno. Ndinawamva akuti, ‘Tiyeni tipite ku Dotani.’ ” Choncho Yosefe analondola abale ake ndipo anakawapeza ku Dotani. Onani mutuwo |