Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 37:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Kodi abale ako sadyetsa zoweta mu Sekemu? Tiyeni, ndikutuma iwe kwa iwo. Ndipo anati, Ndine pano.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Kodi abale ako sadyetsa zoweta m'Sekemu? Tiyeni, ndikutuma iwe kwa iwo. Ndipo anati, Ndine pano.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Israele adauza Yosefe kuti, “Abale ako akuŵeta nkhosa ku Sekemu. Ndikufuna kuti upite kwa iwowo.” Yosefe adayankha kuti, “Chabwino, atate.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 ndipo Israeli anati kwa Yosefe, “Tsono, ndikufuna kukutuma kwa abale ako.” Iye anayankha nati, “Chabwino.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 37:13
13 Mawu Ofanana  

Ndipo panali zitapita zimenezo, Mulungu anamuyesa Abrahamu nati kwa iye, Abrahamu; ndipo anati, Ndine pano.


Koma mthenga wa Yehova anamuitana iye ndi mau odzera kumwamba, nati, Abrahamu, Abrahamu; ndi iye anati, Ndine pano.


Ndipo panali atakalamba Isaki, ndi maso ake anali akhungu losaona nalo, anamuitana Esau mwana wake wamwamuna wamkulu, nati kwa iye, Mwana wanga; ndipo anati kwa iye, Ndine pano.


Ndipo iye analowa kwa atate wake, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga?


Ndipo Yakobo anafika ndi mtendere kumzinda wa Sekemu umene uli m'dziko la Kanani, pamene anachokera ku Padanaramu; namanga tsasa pandunji pa mzindapo.


Ndipo abale ake ananka kukaweta zoweta za atate wao mu Sekemu.


Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.


Ndipo mwini mundawo anati, Ndidzachita chiyani? Ndidzatuma mwana wanga amene ndikondana naye; kapena akamchitira iye ulemu.


Pamenepo Eli anaitana Samuele, nati, Mwana wanga, Samuele. Nati iye, Ndine.


Ndipo Yehova anabwereza kumuitana Samuele nthawi yachitatu. Ndipo iye anauka napita kwa Eli, nati, Ndine, pakuti mwandiitana ndithu. Ndipo Eli anazindikira kuti ndiye Yehova amene analikuitana mwanayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa