Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 36:23 - Buku Lopatulika

23 Ana a Sobala ndi awa: Alivani ndi Manahati ndi Ebala, Sefo ndi Onamu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ana a Sobala ndi awa: Alivani ndi Manahati ndi Ebala, Sefo ndi Onamu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ana a Sobali ndi aŵa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ana aamuna a Sobala anali awa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:23
3 Mawu Ofanana  

Ndi ana a Lotani anali Hori ndi Hemani: mlongo wake wa Lotani anali Timna.


Ana a Zibiyoni ndi amenewa: Aiya ndi Ana; ameneyo ndiye Ana uja anapeza akasupe a madzi amoto m'chipululu, pakudyetsa abulu a Zibiyoni atate wake.


Ana a Sobala: Aliyani, ndi Manahati, ndi Ebala, Sefi, ndi Onamu. Ndi ana a Zibiyoni: Aiya ndi Ana.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa