Genesis 36:22 - Buku Lopatulika22 Ndi ana a Lotani anali Hori ndi Hemani: mlongo wake wa Lotani anali Timna. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndi ana a Lotani anali Hori ndi Hemani: mlongo wake wa Lotani anali Timna. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ana a Lotani anali Hori ndi Hemani, ndipo Timna anali mlongo wa Lotani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ana aamuna a Lotani anali awa: Hori ndi Homamu. Timna anali mlongo wake wa Lotani. Onani mutuwo |