Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 36:16 - Buku Lopatulika

16 mfumu Kora, mfumu Gatamu, mfumu Amaleke: amenewa ndi mafumu a kwa Elifazi m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Ada.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 mfumu Kora, mfumu Gatamu, mfumu Amaleke: amenewa ndi mafumu a kwa Elifazi m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana amuna a Ada.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Gatamu ndi Amaleke. Ameneŵa ndi mafumu mwa ana a Elifazi m'dziko la Edomu. Onseŵa anali ana a Ada.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Kora, Gatamu, ndi Amaleki. Awa anali mafumu mwa ana a Elifazi ku Edomu ndipo onsewa anali zidzukulu za Ada.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:16
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Timna anali mkazi wake wamng'ono wa Elifazi mwana wamwamuna wa Esau; ndipo anambalira Elifazi Amaleke: amenewa ndi ana aamuna a Ada mkazi wake wa Esau.


Amenewa ndi mafumu a ana aamuna a Esau: ana aamuna a Elifazi woyamba wa Esau: mfumu Temani, mfumu Omara, mfumu Zefo, mfumu Kenazi,


Amenewa ndi ana aamuna a Reuwele mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reuwele m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Basemati mkazi wake wa Esau.


Pamenepo mafumu a Edomu anadabwa; agwidwa nako kunthunthumira amphamvu a ku Mowabu; okhala mu Kanani onse asungunuka mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa