Genesis 36:17 - Buku Lopatulika17 Amenewa ndi ana aamuna a Reuwele mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reuwele m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Basemati mkazi wake wa Esau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Amenewa ndi ana amuna a Reuwele mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reuwele m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Basemati mkazi wake wa Esau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mwa ana a Reuele, mwana wa Esau, panali mafumu aŵa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Ameneŵa ndiwo mafumu mwa ana a Ruwele m'dziko la Edomu, ndiponso ndiwo ana a Basemati mkazi wa Esau. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mwa ana a Reueli, mwana wa Esau munali mafumu awa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Awa anali mafumu mwa ana a Reueli ku Edomu. Iwowa anali zidzukulu za Basemati mkazi wa Esau. Onani mutuwo |