Genesis 36:10 - Buku Lopatulika10 amenewa ndi maina a ana aamuna a Esau: Elifazi mwana wamwamuna wa Ada, mkazi wake wa Esau, Reuwele mwana wamwamuna wa Basemati mkazi wake wa Esau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 amenewa ndi maina a ana amuna a Esau: Elifazi mwana wamwamuna wa Ada, mkazi wake wa Esau, Reuwele mwana wamwamuna wa Basemati mkazi wake wa Esau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Maina a ana aamuna a Esau naŵa: Elifazi mwana wa Ada mkazi wa Esau, ndi Reuele mwana wa Basemati mkazi wa Esau. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Awa ndi mayina a ana aamuna a Esau: Elifazi, mwana wa Ada, mkazi wa Esau, ndi Reueli, mwana wamwamuna wa Basemati, mkazi wa Esau. Onani mutuwo |