Genesis 36:9 - Buku Lopatulika9 Mibadwo ya Esau atate wao wa Aedomu m'phiri la Seiri ndi iyi: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mibadwo ya Esau atate wao wa Aedomu m'phiri la Seiri ndi iyi: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Nazi zidzukulu za Esau, kholo la Aedomu, okhala m'dziko lamapiri la Seiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Nazi zidzukulu za Esau, kholo la Aedomu amene ankakhala ku Seiri. Onani mutuwo |