Genesis 34:9 - Buku Lopatulika9 Mukwatirane ndi ife: tipatseni ife ana anu akazi, ndiponso dzitengereni ana athu aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mukwatirane ndi ife: tipatseni ife ana anu akazi, ndiponso dzitengereni ana athu akazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tiyeni tikhale ogwirizana chifukwa cha ukwati umenewu. Ife tidzakwatira ana anu, inunso mudzakwatira ana athu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tiyeni tichite mgwirizano wa ukwati kuti ife tidzikwatira ana anu ndi inu mudzikwatira ana athu. Onani mutuwo |