Genesis 34:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Hamori ananena ndi iwo, kuti, Mtima wa Sekemu mwana wanga umkhumba mwana wako wamkazi: umpatsetu kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Hamori ananena ndi iwo, kuti, Mtima wa Sekemu mwana wanga umkhumba mwana wako wamkazi: umpatsetu kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Hamori adaŵauza kuti, “Mwana wanga Sekemu wamkonda mwana wanu. Chonde muloleni kuti amukwatire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Koma Hamori anawawuza kuti, “Mwana wanga Sekemu wamukonda kwambiri mwana wanu. Chonde muloleni kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwo |