Genesis 34:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mudzakhala pamodzi ndi ife, dziko lidzakhala pamaso panu; khalani m'menemo ndi kuchita malonda, ndi kukhala nazo zanuzanu m'menemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mudzakhala pamodzi ndi ife, dziko lidzakhala pamaso panu; khalani m'menemo ndi kuchita malonda, ndi kukhala nazo zanuzanu m'menemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mukhale nafe pamodzi m'dziko mwathu mommuno. Mukhazikike kulikonse kumene mungakonde, muzichita malonda mwaufulu, ndipo muzigula malo omangira nyumba monga mufunira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Khazikikani pakati pathu. Mukhoza kupeza malo wokhala kulikonse kumene mufuna. Mukhozanso kuchita malonda momasuka ndi kupeza chuma.” Onani mutuwo |