Genesis 34:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Sekemu anati kwa atate wake wa mkazi ndi kwa abale ake, Tipeze ufulu pamaso panu, chimene mudzanena kwa ine ndidzapereka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Sekemu anati kwa atate wake wa mkazi ndi kwa abale ake, Tipeze ufulu pamaso panu, chimene mudzanena kwa ine ndidzapereka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pambuyo pake Sekemu adauza atate ake a Dina ndi alongo ake aja kuti, “Mundikomere mtima, ndipo ndidzakupatsani zonse zimene mungafune. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pamenepo Sekemu anati kwa abambo ndi alongo ake a Dina, “Inu mundikomere mtima, ndipo ndidzakupatsani chilichonse munganene. Onani mutuwo |