Genesis 34:23 - Buku Lopatulika23 Kodi ng'ombe zao ndi chuma chao ndi zoweta zao sizidzakhala zathu? Pokhapo tivomerezana nao ndipo adzakhala pamodzi ndi ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Kodi ng'ombe zao ndi chuma chao ndi zoweta zao sizidzakhala zathu? Pokhapo tivomerezana nao ndipo adzakhala pamodzi ndi ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Nanga sindiye kuti zoŵeta zao, katundu wao ndi ng'ombe zao zidzakhala zathu? Motero tiyeni tivomere kuti azikhala pakati pathu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Tikatero, ndiye kuti ziweto zawo zonsezi, katundu wawo yenseyu ndi ziweto zawo zina zonsezi zidzakhala zathu. Choncho tiyeni tiwavomereze ndipo adzakhazikika pakati pathu.” Onani mutuwo |