Genesis 34:18 - Buku Lopatulika18 Mau ao ndipo anakomera Hamori ndi Sekemu mwana wake wa Hamori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Mau ao ndipo anakomera Hamori ndi Sekemu mwana wake wa Hamori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mau ameneŵa adakondweretsa kwambiri Hamori ndi mwana wake Sekemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mawu amenewa anakondweretsa Hamori ndi mwana wake Sekemu. Onani mutuwo |