Genesis 34:17 - Buku Lopatulika17 Koma mukapanda kutimvera ndi kusadulidwa, pamenepo tidzatenga mwana wathu wamkazi, ndi kumuka naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma mukapanda kutimvera ndi kusadulidwa, pamenepo tidzatenga mwana wathu wamkazi, ndi kumuka naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma ngati simuvomereza zimene tikunenazi, zoti muumbalidwe, ife tidzangomtenga mwana wathu wamkaziyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma ngati simuvomereza kuchita mdulidwe titenga mlongo wathu ndi kupita.” Onani mutuwo |