Genesis 34:16 - Buku Lopatulika16 pamenepo tidzakupatsani inu ana athu aakazi, ndipo tidzadzitengera ana anu aakazi, ndipo tidzakhala pamodzi ndi inu, ndi kukhala mtundu umodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 pamenepo tidzakupatsani inu ana athu akazi, ndipo tidzadzitengera ana anu akazi, ndipo tidzakhala pamodzi ndi inu, ndi kukhala mtundu umodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pamenepo tidzakulolani kuti mukwatire ana athu, ndipo ifenso tidzakwatira ana anu. Tsono tidzakhazikika pakati panu ndi kusanduka fuko limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kenaka tidzakulolani kuti mukwatire ana athu, ifenso tizikwatira ana anu. Choncho tidzakhala pakati panu ndipo tidzakhala anthu amodzi. Onani mutuwo |