Genesis 34:15 - Buku Lopatulika15 Koma apa pokha tidzakuvomerezani: ngati mudzakhala onga ife ndi kudulidwa amuna onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma apa pokha tidzakuvomerezani: ngati mudzakhala onga ife ndi kudulidwa amuna onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tingathe kuvomera pokhapokha inu mutakhala monga momwe tiliri ifemu, ndiye kuti mutaumbala ana anu onse aamuna. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Tikuvomerani pokhapokha mutakhala ngati ife, mutachita mdulidwe ana anu onse aamuna. Onani mutuwo |