Genesis 34:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Dina mwana wamkazi wa Leya, amene anambalira Yakobo, ananka kukaona akazi a kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Dina mwana wamkazi wa Leya, amene anambalira Yakobo, ananka kukaona akazi a kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Dina mwana wa Yakobe wobadwa kwa Leya, adapita kukacheza ndi akazi ena am'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsopano Dina, mwana amene Leya anaberekera Yakobo, anapita kukacheza ndi akazi ena a mʼdzikolo. Onani mutuwo |