Genesis 33:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anati, Nanga khamu lonse limene ndinakomana nalo nlotani? Ndipo anati, Kuti ndipeze ufulu pamaso pa mbuyanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anati, Nanga khamu lonse limene ndinakomana nalo nlotani? Ndipo anati, Kuti ndipeze ufulu pamaso pa mbuyanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Esau adati, “Nanga gulu la zoŵeta ndakumana nalo lija ndi lachiyani?” Yakobe adayankha kuti, “Mbuyanga, gulu limene lija ndi lanu, kuti inuyo mundikomere mtima.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Esau anafunsa kuti, “Kodi gulu la ziweto ndakumana nalo lija ndi layani?” Yakobo anayankha nati, “Mbuye wanga, gulu lija ndi lanu kuti mundikomere mtima.” Onani mutuwo |