Genesis 33:7 - Buku Lopatulika7 Ndiponso Leya ndi ana ake anayandikira nawerama pansi: pambuyo pake anayandikira Yosefe ndi Rakele, nawerama pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndiponso Leya ndi ana ake anayandikira nawerama pansi: pambuyo pake anayandikira Yosefe ndi Rakele, nawerama pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adabweranso Leya pamodzi ndi ana ake, ndipo wotsirizira anali Rakele. Onsewo adagwada pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka, Leya ndi ana ake anabwera. Nawonso anaweramitsa mitu pansi. Potsiriza pa onse anabwera Yosefe ndi Rakele naweramitsanso mitu yawo pansi. Onani mutuwo |