Genesis 33:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo adzakazi anayandikira ndi ana ao, nawerama pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo adzakazi anayandikira ndi ana ao, nawerama pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono adzakazi aja adadza pamodzi ndi ana ao, nagwada pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Tsono antchito aja anayandikira naweramitsa mitu pansi. Onani mutuwo |