Genesis 33:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anaika adzakazi ndi ana ao patsogolo, ndi Leya ndi ana ake pambuyo pao, ndi Rakele ndi Yosefe pambuyo pa onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anaika adzakazi ndi ana ao patsogolo, ndi Leya ndi ana ake pambuyo pao, ndi Rakele ndi Yosefe pambuyo pa onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adatsogoza adzakaziwo pamodzi ndi ana ao. Leya ndi ana ake ankatsata pambuyo pao, Rakele ndi Yosefe ankadza pambuyo penipeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anayika antchito ndi ana awo patsogolo, kenaka nʼkubwera Leya ndi ana ake, ndipo pambuyo pawo Rakele ndi Yosefe. Onani mutuwo |