Genesis 33:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo iye mwini anatsogolera patsogolo pao, nawerama pansi kasanu ndi kawiri mpaka anayandikira mkulu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo iye mwini anatsogolera patsogolo pao, nawerama pansi kasanu ndi kawiri mpaka anayandikira mkulu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yakobe adatsogola, ndipo adaŵerama mpaka pansi kasanu ndi kaŵiri akuyandikira mbale wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye mwini anakhala patsogolo nawerama mpaka kukhudza pansi kasanu ndi kawiri pamene amayandikira mʼbale wake. Onani mutuwo |