Genesis 33:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yakobo anatukula maso ake, taonani, anadza Esau, ndi pamodzi naye anthu mazana anai. Ndipo anagawira ana kwa Leya, ndi kwa Rakele, ndi kwa adzakazi awiri aja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yakobo anatukula maso ake, taonani, anadza Esau, ndi pamodzi naye anthu mazana anai. Ndipo anagawira ana kwa Leya, ndi kwa Rakele, ndi kwa adzakazi awiri aja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yakobe adaona Esau akubwera ndi anthu ake 400. Motero ana ake aja adaŵagaŵira Leya, Rakele ndi adzakazi aŵiri aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yakobo atakweza maso ake anaona Esau akubwera ndi anthu ake 400. Choncho ana ake anawagawira Leya, Rakele ndi antchito awiri aja. Onani mutuwo |