Genesis 33:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Esau anabwerera tsiku lomwelo kunka ku Seiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Esau anabwera tsiku lomwelo kunka ku Seiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Motero pa tsiku limenelo Esau adanyamuka ulendo kubwerera ku Seiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Choncho tsiku limenelo Esau anayamba ulendo wobwerera ku Seiri. Onani mutuwo |