Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 33:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo Esau anati, Tiyeni timuke; nditsogolera ndine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo Esau anati, Tiyeni timuke; nditsogolera ndine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndipo Esau adati, “Tiyeni tinyamuke, tizipita. Ine nditsogolako.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndipo Esau anati, “Tiyeni tizipita; nditsagana nanu.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 33:12
2 Mawu Ofanana  

Landiranitu mdalitso wanga umene wafika kwa inu, pakuti Mulungu wandichitira ine zaufulu, ndipo zanganso zindikwanira. Ndipo anamkakamiza, nalandira.


Ndipo anati kwa iye, Mbuyanga adziwa kuti ana ali anthete, ndipo nkhosa ndi zoweta ndili nazo zilinkuyamwitsa: ndipo akathamangitsa tsiku limodzi zoweta zonse zidzafa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa