Genesis 31:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo inu mudziwa kuti ndi mphamvu zanga zonse ndatumikira atate wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo inu mudziwa kuti ndi mphamvu zanga zonse ndatumikira atate wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nonse aŵirinu mukudziŵa bwino kuti ndidagwira ntchito kwa bambo wanu ndi mphamvu zanga zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Inu mukudziwa kuti ndagwirira ntchito abambo anu ndi mphamvu zanga zonse, Onani mutuwo |