Genesis 31:52 - Buku Lopatulika52 Muluwu ndiwo mboni, choimiritsachi ndicho mboni, kuti ine sindidzapitirira pa muluwu kunka kwa iwe, ndipo iwe sudzapitirira pa muluwu ndi pa choimiritsachi kudza kwa ine kuti tichitirane zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Muluwu ndiwo mboni, choimiritsachi ndicho mboni, kuti ine sindidzapitirira pa muluwu kunka kwa iwe, ndipo iwe sudzapitirira pa muluwu ndi pa choimiritsachi kudza kwa ine kuti tichitirane zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Mulu umenewu pamodzi ndi mwala wachikumbutsowu, zonsezi ndi mboni. Ine sindidzapyola mulu umenewu kuti ndilimbane nawe. Iwenso usadzapyole muluwu kuti ulimbane ndi ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Mulu wa miyala uwu ndi chipilalachi ndi mboni. Ine sindidzadutsa mulu wa miyalawu kudzalimbana ndi iwe. Iwenso usadzadutse mulu wa miyalawu kudzalimbana nane. Onani mutuwo |