Genesis 31:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo Labani anati kwa Yakobo. Taona muluwu, taona choimiritsachi, ndachiimiritsa pakati pathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo Labani anati kwa Yakobo. Taona muluwu, taona choimiritsachi, ndachiimiritsa pakati pathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Tsono Labani adauza Yakobe kuti, “Pano pali miyala imene ndaunjika pakati pathu, ndipo pompano pali mwala wachikumbutso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Labani anatinso kwa Yakobo, “Taona pano pali miyala ndi chipilala chimene ndayimika pakati pa iwe ndi ine. Onani mutuwo |