Genesis 31:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yakobo anatumiza naitana Rakele ndi Leya adze kubusa ku zoweta zake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yakobo anatumiza naitana Rakele ndi Leya adze kubusa ku zoweta zake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono Yakobe adatumiza mau kwa Rakele ndi kwa Leya kuti akakumane naye kubusa kumene kunali zoŵeta zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho Yakobo anatumiza mawu kukayitana Rakele ndi Leya kuti abwere ku busa kumene ankaweta ziweto zake. Onani mutuwo |