Genesis 30:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Rakele anati, Ndi malimbano a Mulungu ndalimbana naye mkulu wanga, ndipo ndapambana naye; ndipo anamutcha dzina lake Nafutali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Rakele anati, Ndi malimbano a Mulungu ndalimbana naye mkulu wanga, ndipo ndapambana naye; ndipo anamutcha dzina lake Nafutali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamenepo Rakele adati, “Ndalimbana naye kwambiri mkulu wanga, ndipo ndapambana.” Motero mwanayo adamutcha Nafutali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamenepo Rakele anati, “Ndakhala ndikulimbana kwambiri ndi mʼbale wanga ndipo ndapambana.” Choncho anamutcha Nafutali. Onani mutuwo |