Genesis 30:9 - Buku Lopatulika9 Pamene Leya anaona kuti analeka kubala, anatenga Zilipa mdzakazi wake, nampatsa iye kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamene Leya anaona kuti analeka kubala, anatenga Zilipa mdzakazi wake, nampatsa iye kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Leya ataona kuti waleka kubala, adapereka mdzakazi wake Zilipa kwa Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pamene Leya anaona kuti waleka kubereka ana, iye anatenga wantchito wake Zilipa namupereka kwa Yakobo kuti alowane naye. Onani mutuwo |