Genesis 30:42 - Buku Lopatulika42 Koma pamene ziweto zinali zofooka, sanaziike zimenezo: ndipo zofooka, zinali za Labani, ndi zolimba zinali za Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Koma pamene ziweto zinali zofooka, sanaziike zimenezo: ndipo zofooka, zinali za Labani, ndi zolimba zinali za Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Choncho zoŵeta zikakhala zofooka zinali za Labani, koma zamphamvu zinali za Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Koma sankayika nthambizo pamene ziweto zofowoka zazikazi zinkakweredwa pakumwa madzi. Choncho ziweto zofowoka zonse zinakhala za Labani, ndi ziweto zamphamvu zinakhala za Yakobo. Onani mutuwo |