Genesis 30:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo panali pamene zoweta zolimba zidatenga mabere, Yakobo anaika nthyole pamaso pa zoweta m'micheramo kuti zitenge mabere pa nthyolezo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo panali pamene zoweta zolimba zidatenga mabere, Yakobo anaika nthyole pamaso pa zoweta m'micheramo kuti zitenge mabere pa nthyolezo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Zoŵeta zamphamvu zikamakwerewa, Yakobe ankazikhazikira nthambi zija kumaso kwake pa malo omwera, kuti pakutero zitenge maŵere pafupi ndi nthambizo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Yakobo ankayika nthambi zija momwera madzi pamene ziweto zamphamvu zazikazi zinkakweredwa pofuna kuti zitenge mawere pakumwa madzi moyangʼanana ndi nthambi zija. Onani mutuwo |