Genesis 30:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo iye yekha anatalikitsana ndi Yakobo ulendo wa masiku atatu: ndipo Yakobo anadyetsa ziweto zina za Labani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo iye yekha anatalikitsana ndi Yakobo ulendo wa masiku atatu: ndipo Yakobo anadyetsa ziweto zina za Labani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Atatero adasiyana naye Yakobe uja nayenda mtunda wa masiku atatu. M'menemo nkuti Yakobeyo akuŵeta zoŵeta zina za Labani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Kenaka Labani anayenda mtunda wa masiku atatu kutalikirana ndi Yakobo koma Yakobo anapitiriza kuweta nkhosa zina zonse za Labani. Onani mutuwo |