Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 30:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo Mulungu anakumbukira Rakele, ndipo Mulungu anamvera iye, natsegula m'mimba mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo Mulungu anakumbukira Rakele, ndipo Mulungu anamvera iye, natsegula m'mimba mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono Mulungu adakumbukira Rakele, namva pemphero lake, nkulola kuti abale ana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Kenaka, Mulungu anakumbukira Rakele namva pemphero lake ndi kulola kuti akhale ndi mwana.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 30:22
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Isaki anampembedzera mkazi wake kwa Yehova popeza anali wouma: ndipo Yehova analola kupembedza kwake, ndipo Rebeka mkazi wake anatenga pakati.


Pamene Yehova anaona kuti anamuda Leya, anatsegula m'mimba mwake; koma Rakele anali wouma.


Ndipo Yakobo anapsa mtima ndi Rakele; nati, Kodi ine ndikhala m'malo a Mulungu amene akukaniza iwe zipatso za mimba?


Pambuyo pake ndipo anabala mwana wamkazi, namutcha dzina lake Dina.


ana aamuna a Rakele: ndiwo Yosefe ndi Benjamini;


Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi;


Popeza anakumbukira mau ake oyera, ndi Abrahamu mtumiki wake.


Asungitsa nyumba mkazi wosaona mwana, akhale mai wokondwera ndi ana. Aleluya.


Taonani, ana ndiwo cholowa cha kwa Yehova; chipatso cha m'mimba ndicho mphotho yake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa