Genesis 30:21 - Buku Lopatulika21 Pambuyo pake ndipo anabala mwana wamkazi, namutcha dzina lake Dina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pambuyo pake ndipo anabala mwana wamkazi, namutcha dzina lake Dina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pambuyo pake adabala mwana wamkazi, namutcha Dina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Patapita nthawi Leya anabereka mwana wamkazi ndipo anamutcha Dina. Onani mutuwo |