Genesis 30:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Zilipa mdzakazi wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna wachiwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Zilipa mdzakazi wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna wachiwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Zilipa mdzakazi wa Leyayo adamubaliranso Yakobe mwana wamwamuna wachiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Zilipa, wantchito wa Leya anamubalira Yakobo mwana wa mwamuna wachiwiri. Onani mutuwo |