Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 30:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo Leya anati, Wamwai ine! Ndipo anamutcha dzina lake Gadi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Leya anati, Wamwai ine! Ndipo anamutcha dzina lake Gadi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono Leya adati, “Ndachita mwai.” Motero mwanayo adamutcha Gadi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Pamenepo Leya anati, “Mwayi wangawo!” Choncho anamutcha Gadi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 30:11
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Zilipa mdzakazi wake wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna.


Ndipo Zilipa mdzakazi wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna wachiwiri.


ndipo ana aamuna a Zilipa mdzakazi wake wa Leya: ndiwo Gadi ndi Asere: amenewo ndi ana aamuna a Yakobo amene anabala iye mu Padanaramu.


Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.


Ndi Gadi, achifwamba adzampsinja iye; koma iye adzapsinja pa chitendeni chao.


Koma inu amene mwasiya Yehova, amene mwaiwala phiri langa lopatulika, ndi kukonzera mulungu wamwai gome, ndi kudzazira mulungu waimfa zikho za vinyo wosakaniza;


A ana a Gadi, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa