Genesis 3:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anatseguka maso ao a onse awiri, nadziwa kuti anali amaliseche: ndipo adasoka masamba amkuyu, nadzipangira matewera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anatseguka maso ao a onse awiri, nadziwa kuti anali amaliseche: ndipo adasoka masamba amkuyu, nadzipangira matewera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Atangodya choncho, adazindikira kuti ali maliseche. Choncho adasoka masamba a mkuyu navala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka maso awo anatsekuka, ndipo anazindikira kuti anali maliseche. Choncho anasoka masamba a mkuyu nadzipangira zovala. Onani mutuwo |