Genesis 3:4 - Buku Lopatulika4 Njokayo ndipo inati kwa mkaziyo, Kufa simudzafai; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Njokayo ndipo inati kwa mkaziyo, Kufa simudzafai; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma njokayo idayankha mkaziyo kuti, “Iyai, kufa simudzafa konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Ndithudi simudzafa,” inatero njokayo kwa mkaziyo. Onani mutuwo |
Ndipo inanena naye, Munthu anakwera kukomana nafe, nati kwa ife, Kabwerereni kwa mfumu imene inakutumani inu, nimunene nayo, Atero Yehova, Kodi ndi popeza palibe Mulungu mwa Israele, kuti ulikutuma kukafunsira kwa Baala-Zebubi mulungu wa ku Ekeroni? Chifukwa chake sudzatsika pakama pamene wakwerapo, koma udzafa ndithu.