Genesis 3:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake, Heva; chifukwa ndiye amake wa amoyo onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake, Heva; chifukwa ndiye amake wa amoyo onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Adamu adatcha mkazi wake Heva, chifukwa choti iyeyu anali mai wa anthu onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Munthu uja anatcha mkazi wake Hava, chifukwa iyeyu adzakhala mayi wa anthu onse amoyo. Onani mutuwo |