Genesis 3:21 - Buku Lopatulika21 Yehova Mulungu ndipo anapangira Adamu ndi mkazi wake malaya azikopa, nawaveka iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Yehova Mulungu ndipo anapangira Adamu ndi mkazi wake malaya azikopa, nawaveka iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndipo Chauta adasokera Adamu ndi mkazi wake zovala zachikopa naŵaveka onse aŵiriwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Yehova Mulungu anapangira Adamu ndi mkazi wake zovala zachikopa ndipo anawaveka. Onani mutuwo |