Genesis 29:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anati kwa iwo, Kodi ali bwino? Nati, Ali bwino: taonani, Rakele mwana wake wamkazi alinkudza nazo nkhosa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anati kwa iwo, Kodi ali bwino? Nati, Ali bwino: taonani, Rakele mwana wake wamkazi alinkudza nazo nkhosa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adaŵafunsanso kuti, “Kodi ali bwino?” Iwowo adayankha kuti, “Ee, ali bwino. Suuyu Rakele, mwana wake, akubwera ndi nkhosayu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo Yakobo anawafunsanso, “Kodi ali bwino?” Iwo anati, “Inde ali bwino. Nayu Rakele mwana wake akubwera apoyu ndi nkhosa.” Onani mutuwo |