Genesis 29:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo iye anati, Taonani, kukali msana, si nthawi yosonkhanitsa zoweta; mwetsani nkhosa, pitani, kadyetseni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo iye anati, Taonani, kukali msana, si nthawi yosonkhanitsa zoweta; mwetsani nkhosa, pitani, kadyetseni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono Yakobe adati, “Popeza kuti kukali masana, ndipo nthaŵi yokazilonga sinakwane, bwanji osati muzimwetse madzi, muzitengenso kukazidyetsa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anati, “Taonani, dzuwa likanalipo ndipo nthawi yosonkhanitsa nkhosa sinakwane. Bwanji osazimwetsa madzi nkhosazi.” Onani mutuwo |